Genesis 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+ Rute 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anapitiriza ulendo wawo mpaka anafika ku Betelehemu.+ Atangofika ku Betelehemu, anthu mumzinda wonsewo anayamba kulankhula za iwo.+ Akazi anali kufunsa kuti: “Kodi si Naomi+ uyu?” Rute 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+ Mateyu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa Yudeya m’masiku a mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi+ ochokera kumadera a kum’mawa anabwera ku Yerusalemu. Yohane 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+
19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+
19 Ndipo anapitiriza ulendo wawo mpaka anafika ku Betelehemu.+ Atangofika ku Betelehemu, anthu mumzinda wonsewo anayamba kulankhula za iwo.+ Akazi anali kufunsa kuti: “Kodi si Naomi+ uyu?”
4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+
2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa Yudeya m’masiku a mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi+ ochokera kumadera a kum’mawa anabwera ku Yerusalemu.
42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+