1 Samueli 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzavula zovala anthu ophedwa,+ anapeza Sauli ndi ana ake atatu atafa paphiri la Giliboa.+
8 Ndiyeno tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzavula zovala anthu ophedwa,+ anapeza Sauli ndi ana ake atatu atafa paphiri la Giliboa.+