Genesis 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake Debora+ mlezi wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli m’munsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautcha kuti Aloni-bakuti.*
8 Pambuyo pake Debora+ mlezi wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli m’munsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautcha kuti Aloni-bakuti.*