-
1 Mbiri 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Panalinso Salumu mwana wa Kore. Kore anali mwana wa Ebiasafu+ ndipo Ebiasafu anali mwana+ wa Kora.+ Salumu ndi abale ake a nyumba ya makolo ake, Akora,+ anali oyang’anira ntchito pochita utumiki wawo pamodzi ndi makolo awo, monga alonda+ a pachihema pamsasa wa Yehova. Iwo anali alonda a pachipata.
-