Levitiko 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu asanu mwa inu adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+ Salimo 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Inu mudzandiveka mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo.Mudzakomola ondiukira.+
8 Anthu asanu mwa inu adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+