-
1 Mbiri 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Tsopano awa ndiwo atsogoleri a nyumba ya makolo awo: Eferi, Isi, Elieli, Azirieli, Yeremiya, Hodaviya, ndi Yahadieli. Onsewa anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, amuna amphamvu, olimba mtima, ndiponso otchuka.
-