Yoswa 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maere achinayi anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara potsata mabanja awo.