Deuteronomo 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kwa Aseri anati:+“Aseri ndi wodalitsidwa ndi ana aamuna.+Akhale wovomerezeka ndi abale ake,+Woponda phazi lake m’mafuta.+
24 Kwa Aseri anati:+“Aseri ndi wodalitsidwa ndi ana aamuna.+Akhale wovomerezeka ndi abale ake,+Woponda phazi lake m’mafuta.+