Genesis 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yokesani anabereka Sheba+ ndi Dedani.+ Ana a Dedani anali Asurimu, Letusimu ndi Leumimu. Yesaya 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+
13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+