Yoswa 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero Yehova anakhaladi ndi Yoswa,+ ndipo mbiri yake inamveka padziko lonse lapansi.+