Ekisodo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133. 1 Mbiri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Kohati+ anali Amuramu,+ Izara, Heburoni, ndi Uziyeli.+
18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133.