Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 94:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova akanapanda kundithandiza,+Ndikanatsikira kuli chete mofulumira.+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+