Ekisodo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Usaphe munthu.*+ 2 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli.
4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli.