2 Mafumu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata+ chotchedwa Maziko, ndipo gawo linanso limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata kumbuyo kwa asilikali othamanga. Muzidzasinthana kulondera mosamala nyumbayo.+
6 Gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata+ chotchedwa Maziko, ndipo gawo linanso limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata kumbuyo kwa asilikali othamanga. Muzidzasinthana kulondera mosamala nyumbayo.+