Genesis 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Abulahamu anadzuka m’mawa kwambiri n’kutenga mkate ndi thumba la madzi lachikopa, n’kuziika paphewa pa Hagara.+ Atatero anamuuza kuti azipita limodzi ndi mwana wakeyo.+ Chotero Hagarayo ananyamuka n’kumangoyendayenda m’chipululu cha Beere-seba.*+ 2 Samueli 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kusamutsa ufumu kuuchotsa m’nyumba ya Sauli, n’kukhazikitsa mpando wachifumu wa Davide mu Isiraeli ndi mu Yuda, kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.”+
14 Choncho Abulahamu anadzuka m’mawa kwambiri n’kutenga mkate ndi thumba la madzi lachikopa, n’kuziika paphewa pa Hagara.+ Atatero anamuuza kuti azipita limodzi ndi mwana wakeyo.+ Chotero Hagarayo ananyamuka n’kumangoyendayenda m’chipululu cha Beere-seba.*+
10 ndi kusamutsa ufumu kuuchotsa m’nyumba ya Sauli, n’kukhazikitsa mpando wachifumu wa Davide mu Isiraeli ndi mu Yuda, kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.”+