5 Azipereke kwa ogwira ntchito+ osankhidwa a m’nyumba ya Yehova, kuti akazipereke kwa amene akugwira ntchitoyo m’nyumba ya Yehova, kuti amate ming’alu ya nyumbayo.+
8 M’chaka cha 18+ cha ulamuliro wake, atayeretsa dzikolo ndi nyumba ya Mulungu, iye anatuma Safani+ mwana wa Azaliya, Maaseya mkulu wa mzinda, ndi Yowa mwana wa Yowahazi wolemba zochitika, kuti akakonze+ nyumba ya Yehova Mulungu wake.