2 Mafumu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pofika m’chaka cha 23 cha Mfumu Yehoasi, ansembe anali asanakonzebe ming’alu ya nyumbayo.+ Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+ Mlaliki 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+
4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+
18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+