2 Mafumu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 amisiri omanga ndi miyala, ndi anthu osema miyala.+ Ndalamazo anaguliranso matabwa ndi miyala yosema yokonzera ming’alu ya nyumba ya Yehova ndiponso analipirira zonse zimene anagwiritsa ntchito pokonza nyumbayo.
12 amisiri omanga ndi miyala, ndi anthu osema miyala.+ Ndalamazo anaguliranso matabwa ndi miyala yosema yokonzera ming’alu ya nyumba ya Yehova ndiponso analipirira zonse zimene anagwiritsa ntchito pokonza nyumbayo.