Miyambo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wopanduka amawononga mnzake ndi pakamwa pake,+ koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+ Miyambo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri akamamvera mabodza, onse omutumikira adzakhala oipa.+
9 Wopanduka amawononga mnzake ndi pakamwa pake,+ koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+