1 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+ Yeremiya 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inawayankha kuti: “Taonani! Iye ali m’manja mwanu. Palibe chimene ine mfumu ndingachite motsutsana nanu.”+
11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+
5 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inawayankha kuti: “Taonani! Iye ali m’manja mwanu. Palibe chimene ine mfumu ndingachite motsutsana nanu.”+