Yohane 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo anamupereka kwa iwo kuti akamupachike.+ Tsopano Yesu anakhala m’manja mwawo.