2 Mafumu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza panyumba ya Yehova+ ndi m’nyumba yosungiramo chuma cha mfumu. Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.
14 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza panyumba ya Yehova+ ndi m’nyumba yosungiramo chuma cha mfumu. Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.