Yoswa 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse omwe anali naye anachoka ku Libina n’kupita ku Lakisi.+ Kumeneko anamanga msasa pafupi ndi mzindawo n’kuuthira nkhondo. Mika 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe mkazi wokhala ku Lakisi,+ mangirira galeta ku gulu la mahatchi.* Mzinda umenewu ndiwo unayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti kupanduka kwa Isiraeli kwapezeka mwa iwe.+
31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse omwe anali naye anachoka ku Libina n’kupita ku Lakisi.+ Kumeneko anamanga msasa pafupi ndi mzindawo n’kuuthira nkhondo.
13 Iwe mkazi wokhala ku Lakisi,+ mangirira galeta ku gulu la mahatchi.* Mzinda umenewu ndiwo unayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti kupanduka kwa Isiraeli kwapezeka mwa iwe.+