1 Samueli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000. Yeremiya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu asilikali okwera pamahatchi, mangani mahatchi anu ndi kukwerapo, ndipo muvale zisoti zanu ndi kukhala okonzeka. Pukutani mikondo yanu ing’onoing’ono. Valani zovala zanu zamamba achitsulo.+
5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000.
4 Inu asilikali okwera pamahatchi, mangani mahatchi anu ndi kukwerapo, ndipo muvale zisoti zanu ndi kukhala okonzeka. Pukutani mikondo yanu ing’onoing’ono. Valani zovala zanu zamamba achitsulo.+