Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano Sauli anayamba kuveka Davide zovala zake. Anamuveka chisoti chamkuwa kumutu kwake, komanso chovala chamamba achitsulo.

  • 1 Mafumu 22:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndiyeno munthu wina anakoka uta n’kuponya muvi wake chiponyeponye, koma analasa mfumu ya Isiraeli pampata umene unali pakati pa chovala chake chokhala ndi mamba achitsulo, ndi zovala zake zina zodzitetezera. Choncho mfumuyo inauza woyendetsa galeta lake kuti:+ “Tembenuza dzanja lako ndipo unditulutse m’bwalo lankhondoli, chifukwa ndavulala kwambiri.”

  • 2 Mbiri 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+

  • Yeremiya 51:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo.

      “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena