Oweruza 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya. 1 Samueli 17:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+
16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya.
49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+