Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Benjamini adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ M’mawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zimene wafunkha.”+

  • 1 Samueli 17:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndiyeno anatenga ndodo m’manja mwake ndi kusankha miyala isanu yosalala kwambiri ya m’chigwa.* Iye anaika miyalayi m’chikwama chake cha kubusa mmene anali kusungiramo zinthu, ndipo m’manja mwake munali gulaye.*+ Kenako anayamba kupita kumene kunali Mfilisiti uja.

  • 1 Samueli 17:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+

  • 1 Mbiri 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.

  • 2 Mbiri 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena