-
Oweruza 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Choncho Yehova anawapatsa mpulumutsi, Ehudi,+ munthu wogwiritsa ntchito dzanja lamanzere,+ wa fuko la Benjamini,+ mwana wa Gera. M’kupita kwa nthawi, ana a Isiraeli anatumiza msonkho wawo kwa Egiloni mfumu ya Mowabu, kudzera mwa Ehudi.
-