Oweruza 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 78:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+ Salimo 107:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+ Yeremiya 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Mudzaitanira pa ine komanso mudzabwera ndi kupemphera kwa ine ndipo ine ndidzakumvetserani.’+
9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+
34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+
13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+