Oweruza 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya. 1 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.
16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya.
2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.