-
1 Samueli 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pamenepo Yonatani anavula malaya ake akunja odula manja ndi kupatsa Davide. Anam’patsanso zovala zina ngakhalenso lupanga, uta ndi lamba wake.
-