Esitere 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mwamuna wina, Myuda, anali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+ Mwamunayu dzina lake anali Moredekai+ mwana wa Yairi, mwana wa Simeyi amene anali mwana wa Kisi M’benjamini.+ Esitere 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mfumu Ahasiwero inauza mfumukazi Esitere ndi Moredekai Myuda kuti: “Nyumba ya Hamani ndaipereka kwa Esitere,+ ndipo Hamani wapachikidwa pamtengo+ chifukwa chakuti anatambasula dzanja lake ndi kuukira Ayuda.
5 Tsopano mwamuna wina, Myuda, anali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+ Mwamunayu dzina lake anali Moredekai+ mwana wa Yairi, mwana wa Simeyi amene anali mwana wa Kisi M’benjamini.+
7 Choncho Mfumu Ahasiwero inauza mfumukazi Esitere ndi Moredekai Myuda kuti: “Nyumba ya Hamani ndaipereka kwa Esitere,+ ndipo Hamani wapachikidwa pamtengo+ chifukwa chakuti anatambasula dzanja lake ndi kuukira Ayuda.