21 Pamenepo Sauli anayankha kuti: “Kodi ine si wa m’fuko la Benjamini, fuko laling’ono kwambiri+ pa mafuko onse a Isiraeli?+ Ndipo kodi banja langa sindilo laling’ono kwambiri pa mabanja onse a m’fuko la Benjamini?+ Ndiye n’chifukwa chiyani mwalankhula mawu otere kwa ine?”+