Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 20:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Pamapeto pake, ana a Benjamini onse amene anaphedwa pa tsikulo, anakwana amuna 25,000 ogwira lupanga.+ Onsewa anali amuna amphamvu zawo.

  • Oweruza 20:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi.

  • Oweruza 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kumva chisoni chifukwa cha Benjamini m’bale wawo. Choncho anati: “Lero fuko limodzi ladulidwa ndi kuchotsedwa mu Isiraeli.

  • Salimo 68:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+

      Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,

      Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena