Oweruza 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera. Oweruza 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova anagonjetsa ana a Benjamini+ pamaso pa Aisiraeli, moti pa tsiku limeneli ana a Isiraeli anapha ana a Benjamini 25,100. Onsewa anali amuna ogwira lupanga.+
15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera.
35 Yehova anagonjetsa ana a Benjamini+ pamaso pa Aisiraeli, moti pa tsiku limeneli ana a Isiraeli anapha ana a Benjamini 25,100. Onsewa anali amuna ogwira lupanga.+