Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kwa Benjamini anati:+

      “Wokondedwa+ wa Yehova akhale m’chitetezo cha Mulungu,+

      Pamene akumutchinjiriza tsiku lonse,+

      Ndipo iye akhale pakati pa mapewa ake.”+

  • Oweruza 20:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya.

  • 1 Samueli 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Mawa nthawi ngati ino ndikutumizira munthu kuchokera kudera la Benjamini,+ ndipo udzam’dzoze+ kukhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli. Iye adzapulumutsa anthu anga m’manja mwa Afilisiti,+ chifukwa ndaona kusautsika kwawo ndipo ndamva kulira kwawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena