1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+ 1 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anatuma ine kudzakudzoza+ kukhala mfumu ya anthu ake Aisiraeli, choncho imva zimene Yehova wanena.+ 2 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”
10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+
15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anatuma ine kudzakudzoza+ kukhala mfumu ya anthu ake Aisiraeli, choncho imva zimene Yehova wanena.+
3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”