Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 17:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Azichita zimenezi kuti mtima wake usadzikweze pamaso pa abale ake,+ komanso kuti asachoke pachilamulo mwa kupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Azichita zimenezi kuti iyeyo ndi ana ake atalikitse masiku a ufumu wawo+ mu Isiraeli.

  • 1 Samueli 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngati mudzaopa Yehova,+ n’kumutumikiradi+ ndi kumvera mawu ake,+ ndipo ngati simudzapandukira+ malamulo a Yehova, Yehova Mulungu wanu adzakhala nanu, inuyo pamodzi ndi mfumu yokulamuliraniyo.

  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena