1 Samueli 17:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+
49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+