Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+

  • 2 Samueli 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anthu anayi amenewa anali mbadwa za Arefai ku Gati.+ Iwo anaphedwa ndi dzanja la Davide ndi la atumiki ake.+

  • 2 Samueli 22:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndidzawawononga onse ndi kuwaphwanya zibenthuzibenthu+ kuti asadzukenso.+

      Iwo adzagwa pansi ndipo ndidzawapondaponda ndi mapazi anga.+

  • Salimo 44:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndinu amene munatipulumutsa kwa adani athu,+

      Ndipo munanyazitsa anthu amene amadana nafe kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena