2 Mbiri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziya anaonetsetsa kuti gulu la asilikali lonselo lili ndi zishango, mikondo ingʼonoingʼono,+ zipewa, zovala zamamba achitsulo,+ mauta ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+
14 Uziya anaonetsetsa kuti gulu la asilikali lonselo lili ndi zishango, mikondo ingʼonoingʼono,+ zipewa, zovala zamamba achitsulo,+ mauta ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+