Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 M’mizinda yonse yosiyanasiyana anaikamo zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono.+ Mizindayo anailimbitsa kwambiri, ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.

  • 2 Mbiri 14:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Asa anakhala ndi gulu lankhondo lonyamula zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono,+ la asilikali 300,000 a fuko la Yuda.+ Analinso ndi asilikali onyamula zishango zazing’ono+ ndi odziwa kupinda uta okwanira 280,000+ a fuko la Benjamini. Onsewa anali amuna amphamvu ndi olimba mtima.

  • 2 Mbiri 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako Amaziya anasonkhanitsa Ayuda n’kuwaimiritsa motsatira nyumba ya makolo awo.+ Anawaika m’magulu a anthu 1,000+ ndi mtsogoleri wawo, ndiponso m’magulu a anthu 100+ ndi mtsogoleri wawo, a mafuko a Yuda ndi Benjamini. Iye anawalemba mayina anthuwo, kuyambira azaka 20+ kupita m’tsogolo ndipo anapeza kuti analipo 300,000. Anali amuna ochita kusankhidwa a m’gulu la asilikali, onyamula mkondo waung’ono+ ndi chishango chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena