Salimo 68:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+ Yesaya 60:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+
27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+
22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+