Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Rehobowamu atafika ku Yerusalemu,+ nthawi yomweyo anasonkhanitsa amuna ochita kusankhidwa odziwa kumenya nkhondo okwanira 180,000+ a nyumba yonse ya Yuda ndi ya Benjamini.+ Anawasonkhanitsa kuti akamenyane ndi Isiraeli pofuna kuti ufumu ubwerere kwa Rehobowamu.

  • 2 Mbiri 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho Abiya anapita kukamenya nkhondoyo ndi gulu la amuna amphamvu ankhondo+ osankhidwa mwapadera okwanira 400,000. Yerobowamu nayenso anapita kukamenyana ndi Abiya ndipo anapita ndi asilikali 800,000. Amenewa anali amuna amphamvu ndi olimba mtima osankhidwa mwapadera, ndipo anakafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena