1 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.
2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.