Ekisodo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Aroni azifukiza zofukiza zonunkhira paguwapo.+ M’mawa uliwonse akamasamalira nyale,+ azifukiza zofukizazo.
7 “Aroni azifukiza zofukiza zonunkhira paguwapo.+ M’mawa uliwonse akamasamalira nyale,+ azifukiza zofukizazo.