Ekisodo 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi mkuwa.+ 2 Mafumu 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.
3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi mkuwa.+
14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.