1 Mafumu 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yooneka ngati mbale zolowa+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndi maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.
41 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yooneka ngati mbale zolowa+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndi maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.