1 Mafumu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anapanga maukonde olukanalukana ndiponso zokongoletsera zolukanalukana ngati tcheni,+ za mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo.+ Anapanga zimenezi zokwanira 7 za mutu umodzi, ndi zinanso 7 za mutu winawo.
17 Anapanga maukonde olukanalukana ndiponso zokongoletsera zolukanalukana ngati tcheni,+ za mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo.+ Anapanga zimenezi zokwanira 7 za mutu umodzi, ndi zinanso 7 za mutu winawo.