Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+ Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+ Chivumbulutso 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.
10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+
6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+
5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.